Numeri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene Balamu anakweza maso ake n’kuona Aisiraeli ali m’misasa mwa mafuko awo,+ mzimu wa Mulungu unafika pa iye.+ 2 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova unandilankhulitsa,+Ndipo mawu ake anali palilime langa.+
2 Pamene Balamu anakweza maso ake n’kuona Aisiraeli ali m’misasa mwa mafuko awo,+ mzimu wa Mulungu unafika pa iye.+