Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”