2 Mbiri 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mpingo wonse wa Ayuda,+ ansembe, Alevi+ ndiponso mpingo wonse wa anthu amene anachokera ku Isiraeli,+ alendo+ amene anachokera m’dziko la Isiraeli+ ndi amene anali kukhala m’dziko la Yuda, anapitiriza kusangalala.+
25 Mpingo wonse wa Ayuda,+ ansembe, Alevi+ ndiponso mpingo wonse wa anthu amene anachokera ku Isiraeli,+ alendo+ amene anachokera m’dziko la Isiraeli+ ndi amene anali kukhala m’dziko la Yuda, anapitiriza kusangalala.+