Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 39:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mbuye wakeyo anaona kuti Yehova anali ndi mnyamatayo, ndi kuti chilichonse chimene anali kuchita, Yehova anali kuchidalitsa.

  • 1 Samueli 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Sauli anaona ndi kudziwa kuti Yehova ali ndi Davide.+ Ndipo Mikala, mwana wamkazi wa Sauli, anam’konda kwambiri Davide.+

  • Zekariya 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’masiku amenewo, amuna 10 ochokera m’zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira+ chovala cha munthu amene ndi Myuda+ ndi kunena kuti: “Anthu inu tipita nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+

  • Machitidwe 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena