1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+ 1 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taona! Ine ndikudziwa bwino kwambiri kuti mosalephera iweyo udzalamulira monga mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhazikika m’banja lako nthawi zonse.
13 Choncho Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ ndi kum’dzoza pakati pa abale ake. Zitatero, mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa Davide kuyambira tsiku limenelo mpaka m’tsogolo.+ Kenako Samueli ananyamuka kupita ku Rama.+
20 Taona! Ine ndikudziwa bwino kwambiri kuti mosalephera iweyo udzalamulira monga mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhazikika m’banja lako nthawi zonse.