2 Samueli 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+ 1 Mafumu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Solomo anayamba kuchita zinthu zimene zinali zoipa+ m’maso mwa Yehova, ndipo sanatsatire Yehova ndi mtima wonse ngati Davide bambo ake.+ 1 Mafumu 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abiyamu anapitiriza kuyenda m’machimo onse amene bambo ake anachita. Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+
15 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli+ yense ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo+ kwa anthu ake onse.+
6 Chotero Solomo anayamba kuchita zinthu zimene zinali zoipa+ m’maso mwa Yehova, ndipo sanatsatire Yehova ndi mtima wonse ngati Davide bambo ake.+
3 Abiyamu anapitiriza kuyenda m’machimo onse amene bambo ake anachita. Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+