2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+ 2 Mbiri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amaziya anapitiriza kuchita zolungama pamaso pa Yehova,+ koma osati ndi mtima wathunthu.+ 2 Mbiri 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake. Salimo 119:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Mtima wanga usunge malangizo anu mosalakwitsa kanthu,+Kuti ndisachite manyazi.+
3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+
20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake.