Deuteronomo 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+ 2 Mbiri 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uziya anali kufunafuna+ Mulungu m’masiku a Zekariya yemwe anali kumulangiza kuti aziopa Mulungu woona.+ M’masiku amene iye anafunafuna Yehova, Mulungu woonayo anachititsa kuti zinthu zizimuyendera bwino.+
29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+
5 Uziya anali kufunafuna+ Mulungu m’masiku a Zekariya yemwe anali kumulangiza kuti aziopa Mulungu woona.+ M’masiku amene iye anafunafuna Yehova, Mulungu woonayo anachititsa kuti zinthu zizimuyendera bwino.+