2 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+ Yeremiya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+
6 M’chaka cha 9 cha Hoshiya, mfumu ya Asuri inalanda Samariya+ n’kutenga Aisiraeli kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala+ ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani,+ ndiponso m’mizinda ya Amedi.+
16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+