Ezara 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno ndinawayezera siliva, golide ndi ziwiya.+ Zimenezi zinali zopereka za kunyumba ya Mulungu wathu zimene mfumu,+ aphungu ake,+ akalonga ake ndi Aisiraeli onse+ amene anali kumeneko anapereka.
25 Ndiyeno ndinawayezera siliva, golide ndi ziwiya.+ Zimenezi zinali zopereka za kunyumba ya Mulungu wathu zimene mfumu,+ aphungu ake,+ akalonga ake ndi Aisiraeli onse+ amene anali kumeneko anapereka.