Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 35:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa,+ komanso, aliyense amene anali ndi mzimu wofunitsitsa, anabwera ndipo anabweretsa zopereka kwa Yehova zoti zikagwire ntchito pachihema chokumanako ndi pa utumiki wonse wochitika pamenepo. Anabweretsanso zinthu zopangira zovala zopatulika.

  • 1 Mbiri 29:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+

  • Ezara 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Munyamulenso siliva ndi golide yense amene mum’peze m’chigawo chonse cha Babulo, limodzi ndi mphatso za anthu+ ndi za ansembe omwe akupereka mwaufulu kunyumba ya Mulungu wawo,+ yomwe ili ku Yerusalemu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena