Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uza ana a Isiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Anthu inu mulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene mtima wake wamulimbikitsa.+

  • Ekisodo 36:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Mose anaitana Bezaleli, Oholiabu ndi mwamuna aliyense wa mtima wanzeru amene Yehova anaika nzeru mumtima mwake.+ Anaitana aliyense amene anali ndi mtima wofunitsitsa kugwira ntchitoyi.+

  • 2 Akorinto 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mphatso yochokera pansi pa mtima ndi imene Mulungu amakondwera nayo, chifukwa Mulungu amafuna kuti munthu apereke zimene angathe,+ osati zimene sangathe.

  • 2 Akorinto 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena