Nehemiya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo anapeza kuti m’chilamulo chimene Yehova anawapatsa kudzera mwa Mose+ analembamo kuti ana a Isiraeli azikhala m’misasa+ pa nthawi ya chikondwerero m’mwezi wa 7.+ Yohane 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komabe chikondwerero cha Ayuda, chikondwerero cha misasa+ chinali pafupi.
14 Pamenepo anapeza kuti m’chilamulo chimene Yehova anawapatsa kudzera mwa Mose+ analembamo kuti ana a Isiraeli azikhala m’misasa+ pa nthawi ya chikondwerero m’mwezi wa 7.+