Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa ndi kupita kudziko lina,+ ndipo adzakumverani chifundo+ n’kukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+

  • Nehemiya 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Awa ndi anthu a m’chigawo+ amene anatuluka mu ukapolo+ wa anthu omwe Nebukadinezara+ mfumu ya ku Babulo anawatengera ku ukapolo ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+

  • Zefaniya 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chigawo chimenecho chidzakhala cha otsala a m’nyumba ya Yuda+ ndipo adzapezamo msipu. Madzulo iwo adzagona momasuka m’nyumba za mu Asikeloni. Zidzatero chifukwa chakuti Yehova Mulungu wawo adzawakumbukira+ ndipo adzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu awo omwe anagwidwa n’kutengedwa kupita ku ukapolo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena