Ekisodo 28:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+ 1 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.
40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+
18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.