Salimo 103:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+Kwa anthu amene amamuopa.+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+ Luka 1:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chifundo chake chakhala pa amene amamuopa ku mibadwomibadwo.+
17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+Kwa anthu amene amamuopa.+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+ Luka 1:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chifundo chake chakhala pa amene amamuopa ku mibadwomibadwo.+