Nehemiya 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ine ndinawayankha kuti: “Mulungu wakumwamba+ ndi amene adzatithandiza kuti zinthu zitiyendere bwino,+ ndipo ife atumiki ake tipitiriza kumanga mpandawu. Inu mulibe gawo,+ ufulu kapena chilichonse chokukumbukirani nacho+ mu Yerusalemu.” Yohane 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mayi wachisamariyayo anafunsa Yesu kuti: “Popeza inu ndinu Myuda, bwanji mukupempha madzi akumwa kwa ine, mayi wachisamariya?” (Pakuti Ayuda ndi Asamariya sayanjana.)+ Yohane 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mumalambira chimene simuchidziwa.+ Ife timalambira chimene tikuchidziwa, chifukwa chipulumutso chikuchokera kwa Ayuda.+
20 Koma ine ndinawayankha kuti: “Mulungu wakumwamba+ ndi amene adzatithandiza kuti zinthu zitiyendere bwino,+ ndipo ife atumiki ake tipitiriza kumanga mpandawu. Inu mulibe gawo,+ ufulu kapena chilichonse chokukumbukirani nacho+ mu Yerusalemu.”
9 Mayi wachisamariyayo anafunsa Yesu kuti: “Popeza inu ndinu Myuda, bwanji mukupempha madzi akumwa kwa ine, mayi wachisamariya?” (Pakuti Ayuda ndi Asamariya sayanjana.)+
22 Inu mumalambira chimene simuchidziwa.+ Ife timalambira chimene tikuchidziwa, chifukwa chipulumutso chikuchokera kwa Ayuda.+