Salimo 122:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pemphererani mtendere wa Yerusalemu, anthu inu.+Amene amakukonda, mzinda iwe, sadzakhala ndi nkhawa iliyonse.+ Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+
6 Pemphererani mtendere wa Yerusalemu, anthu inu.+Amene amakukonda, mzinda iwe, sadzakhala ndi nkhawa iliyonse.+
127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+