13 Ndiyeno inu mfumu dziwani kuti, mzinda umenewu ukamangidwanso, mpanda wake n’kumalizidwa, anthu amenewa asiya kupereka msonkho umene munthu aliyense amapereka,+ msonkho wakatundu,+ ndi msonkho wapanjira ndipo zimenezi zidzachititsa kuti chuma+ cha mafumu chiwonongeke.