Zekariya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’mwezi wa 8, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido,+ kuti: Zekariya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu amene ali kutali, ndithu adzabwera kudzamanga nawo kachisi wa Yehova.”+ Anthu inu mukadzamvera mawu a Yehova Mulungu wanu,+ mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma kwa inu.’”+
1 M’mwezi wa 8, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido,+ kuti:
15 Anthu amene ali kutali, ndithu adzabwera kudzamanga nawo kachisi wa Yehova.”+ Anthu inu mukadzamvera mawu a Yehova Mulungu wanu,+ mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma kwa inu.’”+