Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Panali pa nthawi imeneyi pamene ntchito yomanga nyumba ya Mulungu, imene inali ku Yerusalemu, inaima ndipo inakhala chiimire mpaka chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo+ mfumu ya Perisiya.

  • Hagai 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo,+ m’mwezi wa 6, pa tsiku loyamba la mweziwo, mawu a Yehova anafika kwa Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ bwanamkubwa wa Yuda,+ ndi kwa Yoswa+ mwana wa Yehozadaki+ mkulu wa ansembe. Mawuwa anafika kwa anthu amenewa kudzera mwa mneneri Hagai+ kuti:

  • Hagai 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa tsiku la 24 la mwezi wa 9, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo, Yehova analankhula ndi mneneri Hagai+ kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena