Ezara 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Panali pa nthawi imeneyi pamene ntchito yomanga nyumba ya Mulungu, imene inali ku Yerusalemu, inaima ndipo inakhala chiimire mpaka chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo+ mfumu ya Perisiya. Zekariya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’mwezi wa 8, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido,+ kuti:
24 Panali pa nthawi imeneyi pamene ntchito yomanga nyumba ya Mulungu, imene inali ku Yerusalemu, inaima ndipo inakhala chiimire mpaka chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo+ mfumu ya Perisiya.
1 M’mwezi wa 8, m’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya,+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido,+ kuti: