Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova Mulungu wanu adzachita mdulidwe wa mitima yanu+ ndi mitima ya ana anu,+ kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti mukhale ndi moyo.+

  • 2 Mbiri 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+

  • Salimo 78:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+

      M’badwo wosamva ndi wopanduka,+

      M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+

      Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena