2 Mbiri 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 aliyense amene wakonza mtima wake+ kuti afunefune Mulungu woona Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi zinthu zopatulika.”+ Ezara 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 popeza Ezara anakonza+ mtima wake kuti aphunzire chilamulo cha Yehova+ ndi kuchichita+ ndiponso kuti aphunzitse+ mu Isiraeli malamulo+ ndi chilungamo.+
19 aliyense amene wakonza mtima wake+ kuti afunefune Mulungu woona Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi zinthu zopatulika.”+
10 popeza Ezara anakonza+ mtima wake kuti aphunzire chilamulo cha Yehova+ ndi kuchichita+ ndiponso kuti aphunzitse+ mu Isiraeli malamulo+ ndi chilungamo.+