Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ Zekariya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+
4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+