2 Mbiri 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+ Ezara 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 popeza Ezara anakonza+ mtima wake kuti aphunzire chilamulo cha Yehova+ ndi kuchichita+ ndiponso kuti aphunzitse+ mu Isiraeli malamulo+ ndi chilungamo.+ Salimo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+
3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+
10 popeza Ezara anakonza+ mtima wake kuti aphunzire chilamulo cha Yehova+ ndi kuchichita+ ndiponso kuti aphunzitse+ mu Isiraeli malamulo+ ndi chilungamo.+
17 Mudzamva kuchonderera kwa anthu ofatsa,+ inu Yehova.Mudzakonzekeretsa mitima yawo.+Mudzatchera khutu lanu,+