Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+ Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu kuti adziwe Mulungu. Anthuwo ayenera kufunafuna kumva chilamulo kuchokera pakamwa pake,+ pakuti iye ndi mthenga wa Yehova wa makamu.+