Deuteronomo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la chilamulo ichi, kuchokera m’buku limene ansembe achilevi amasunga.+ 2 Mafumu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.
18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la chilamulo ichi, kuchokera m’buku limene ansembe achilevi amasunga.+
8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.