1 Mbiri 2:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima. Nehemiya 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amuna a ku Betelehemu+ ndi ku Netofa,+ 188.
54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima.