54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima.
8 Choncho akuluakulu amenewa anapita kwa Gedaliya ku Mizipa. Mayina awo anali Isimaeli+ mwana wa Netaniya, Yohanani+ ndi Yonatani ana a Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti, ana a Efai Mnetofa,+ Yezaniya+ mwana wa Amaakati+ pamodzi ndi asilikali awo.+