Nehemiya 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Amuna a ku Beti-azimaveti,+ 42. Nehemiya 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ena anachokera ku Beti-giligala+ komanso m’dera la Geba+ ndi la Azimaveti,+ pakuti kumeneko kunali midzi+ imene oimba anamanga kuzungulira Yerusalemu yense.
29 Ena anachokera ku Beti-giligala+ komanso m’dera la Geba+ ndi la Azimaveti,+ pakuti kumeneko kunali midzi+ imene oimba anamanga kuzungulira Yerusalemu yense.