Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+ Nehemiya 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amuna a ku Kiriyati-yearimu,+ Kefira,+ ndi ku Beeroti,+ 743.
17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+