Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+ 1 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20. Izi zili choncho, nyumba yonse ya Isiraeli inayamba kulirira Yehova.+
17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+
2 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20. Izi zili choncho, nyumba yonse ya Isiraeli inayamba kulirira Yehova.+