-
Nehemiya 9:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 “Koma akangokhala pa mtendere, anali kuchitanso zoipa pamaso panu+ ndipo munali kuwasiya m’manja mwa adani awo amene anali kuwapondaponda.+ Zikatero, anali kubweranso kwa inu ndi kupempha thandizo lanu,+ ndipo inu munali kumva muli kumwambako+ ndi kuwapulumutsa mobwerezabwereza, chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+
-