-
Yoswa 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Panalibe mwamuna ndi mmodzi yemwe amene anatsala mu Ai ndi m’Beteli. Onse anapita kukathamangitsa Aisiraeli, moti zipata za mzindawo anangozisiya zosatseka.
-