Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Salimo 120:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Yehova, ndilanditseni ku milomo yonama,+Ndi ku lilime lachinyengo.+