Nehemiya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Tiye tipangane nthawi kuti tikumane+ m’mudzi wina wa m’chigwa cha Ono.”+ Koma anali kundikonzera chiwembu.+
2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Tiye tipangane nthawi kuti tikumane+ m’mudzi wina wa m’chigwa cha Ono.”+ Koma anali kundikonzera chiwembu.+