Deuteronomo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muyenera kudziwa kuti Yehova Mulungu wanu akukupatsani dziko labwinoli osati chifukwa cha kulungama kwanu, pakuti ndinu anthu ouma khosi.+ Machitidwe 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma makolo athu akale anakana kumumvera. M’malomwake, anamukankhira kumbali,+ ndipo mumtima mwawo anabwerera ku Iguputo.+ Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
6 Muyenera kudziwa kuti Yehova Mulungu wanu akukupatsani dziko labwinoli osati chifukwa cha kulungama kwanu, pakuti ndinu anthu ouma khosi.+
39 Koma makolo athu akale anakana kumumvera. M’malomwake, anamukankhira kumbali,+ ndipo mumtima mwawo anabwerera ku Iguputo.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+