1 Samueli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Hana anali kulankhula mumtima mwake.+ Milomo yake inali kugwedera koma sanali kutulutsa mawu. Eli ataona zimenezo anaganiza kuti waledzera.+ Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+ Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+
13 Koma Hana anali kulankhula mumtima mwake.+ Milomo yake inali kugwedera koma sanali kutulutsa mawu. Eli ataona zimenezo anaganiza kuti waledzera.+
6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+