Genesis 24:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Ndisanamalize kulankhula+ mumtima mwanga,+ ndinangoona Rabeka akutuluka mumzindawu, atanyamula mtsuko wake paphewa. Iye anatsikira kukasupe n’kuyamba kutunga madzi.+ Pamenepo ndinamupempha kuti, ‘Chonde ndigawireko madzi ndimwe.’+ Nehemiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poyankha, mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?”+ Nthawi yomweyo ndinapemphera+ kwa Mulungu wakumwamba.+
45 “Ndisanamalize kulankhula+ mumtima mwanga,+ ndinangoona Rabeka akutuluka mumzindawu, atanyamula mtsuko wake paphewa. Iye anatsikira kukasupe n’kuyamba kutunga madzi.+ Pamenepo ndinamupempha kuti, ‘Chonde ndigawireko madzi ndimwe.’+
4 Poyankha, mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?”+ Nthawi yomweyo ndinapemphera+ kwa Mulungu wakumwamba.+