1 Samueli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Hana anali kulankhula mumtima mwake.+ Milomo yake inali kugwedera koma sanali kutulutsa mawu. Eli ataona zimenezo anaganiza kuti waledzera.+ Nehemiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poyankha, mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?”+ Nthawi yomweyo ndinapemphera+ kwa Mulungu wakumwamba.+
13 Koma Hana anali kulankhula mumtima mwake.+ Milomo yake inali kugwedera koma sanali kutulutsa mawu. Eli ataona zimenezo anaganiza kuti waledzera.+
4 Poyankha, mfumuyo inandifunsa kuti: “Ndiye ukufuna chiyani?”+ Nthawi yomweyo ndinapemphera+ kwa Mulungu wakumwamba.+