Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chotero pa tsikuli, Yoswa anawaika+ kukhala otola nkhuni ndi otungira madzi Aisiraeli,+ ndiponso kuti azitola nkhuni ndi kutunga madzi a paguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.

  • Ezara 2:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Anetini+ onse pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.+

  • Ezara 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu+ oti akauze Ido ndi abale ake Anetini+ ku Kasifiyako, kuti atibweretsere atumiki+ a panyumba ya Mulungu wathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena