26 Anetini+ anali kukhala ku Ofeli.+ Iwonso anakonza mpandawo mpaka kukafika ku Chipata cha Kumadzi,+ kum’mawa. Iwo anakonzanso nsanja yotundumukira kunja kwa mpanda.
31 Malikiya amene anali m’gulu la osula golide,+ anakonza mpandawo mpaka kukafika kunyumba ya Anetini+ ndi amalonda,+ kutsogolo kwa Chipata cha Kufufuza* mpaka pachipinda chapadenga cha pakona.