Ezara 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Alevi:+ Ana a Yesuwa,+ a m’nyumba ya Kadimiyeli+ ochokera pakati pa ana a Hodaviya,+ 74. Nehemiya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno panali Alevi awa: Yesuwa,+ Binui,+ Kadimiyeli,+ Serebiya, Yuda ndi Mataniya.+ Mataniya ndi abale akewa anali oyang’anira oimba nyimbo zoyamika Mulungu.
8 Ndiyeno panali Alevi awa: Yesuwa,+ Binui,+ Kadimiyeli,+ Serebiya, Yuda ndi Mataniya.+ Mataniya ndi abale akewa anali oyang’anira oimba nyimbo zoyamika Mulungu.