1 Mbiri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.” Amosi 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukupeka nyimbo zoti muziimba ndi zipangizo za zingwe,+ ndipo mofanana ndi Davide, mukupanga zipangizo zoimbira.+
5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”
5 Inu mukupeka nyimbo zoti muziimba ndi zipangizo za zingwe,+ ndipo mofanana ndi Davide, mukupanga zipangizo zoimbira.+