Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kwa masiku 7, iwo anachita mosangalala chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ pakuti Yehova anawachititsa kusangalala. Iye anatembenuzira+ kwa iwo mtima wa mfumu ya Asuri kuti ilimbitse manja awo pa ntchito yomanga nyumba ya Mulungu woona, Mulungu wa Isiraeli.

  • Hagai 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda, Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse. Choncho iwo anapita kukagwira ntchito panyumba ya Yehova wa makamu, Mulungu wawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena