Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+ Amosi 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+