-
Esitere 7:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako mfumu inabwera kuchokera kumunda wamaluwa wa panyumba ya mfumu ndi kulowanso m’nyumba imene munali phwando la vinyo.+ Pamenepo inaona Hamani atadzigwetsa pampando wokhala ngati bedi+ pamene panali Esitere. Choncho mfumu inati: “Kodi ukufunanso kugwirira mfumukazi ine ndili m’nyumba mom’muno?” Mfumu italankhula,+ Hamani anamuphimba nkhope.
-