-
2 Samueli 21:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma Rizipa mwana wamkazi wa Aya+ anatenga chiguduli+ ndi kuchiyala pamwala kuti azikhala pamenepo, kuyambira kuchiyambi kwa nyengo yokolola kufikira pamene mvula inagwa pamitemboyo kuchokera kumwamba.+ Iye sanalole mbalame+ zam’mlengalenga kutera pamitemboyo masana, ndipo usiku sanalole zilombo zakutchire+ kufikapo.
-
-
Yesaya 58:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kodi kusala kudya kumene ine ndasankha kukhale kotere? Kodi likhale tsiku loti munthu wochokera kufumbi azisautsa moyo wake?+ Kodi likhale tsiku loti munthu aziweramitsa mutu wake ngati udzu, ndiponso loti aziyala chiguduli ngati bedi lake n’kuwazapo phulusa?+ Kodi limeneli ndi limene mumalitcha tsiku losala kudya ndi lovomerezeka kwa Yehova?+
-