Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno pa tsiku lachitatu,+ Esitere anavala zovala zachifumu.+ Kenako anakaima m’bwalo lamkati+ la nyumba ya mfumu moyang’anana ndi nyumba ya mfumuyo. Pa nthawiyi mfumu inali itakhala pampando wake wachifumu m’nyumba yakeyo moyang’anana ndi khomo lolowera m’nyumbayo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena